Mawu a M'munsi
a Pochitira umboni mawu a Mulungu akuti, “moyo wa nyama uli m’magazi,” magazini ina inati: “Mfundo yoti moyo wa nyama uli m’magazi ndi yoona chifukwa selo lililonse la magazi ndi lofunika kuti munthu kapena nyama ikhale ndi moyo.”—Scientific American.