Mawu a M'munsi
c Iwo ankagwiritsa ntchito muyezo wina pogula ndiponso wina pogulitsa, n’cholinga choti apikule motchipa koma agulitse modula kwambiri. Ankagwiritsanso ntchito sikelo ya ndodo yaitali mbali imodzi kapena yolemera kwambiri mbali imodzi n’cholinga choti azibera anthu.