Mawu a M'munsi
b Kuti mudziwe zambiri za mmene mungachitire ndi mwana wamng’ono amene wachotsedwa ndipo akukhalabe pakhomo pomwepo, onani Nsanja ya Olonda ya October 1, 2001, patsamba 16 ndi 17, komanso ya November 15, 1988, tsamba 20, ndiponso Utumiki Wathu wa Ufumu wa August 2002, patsamba 3 ndi 4.