Mawu a M'munsi
a Kusintha kwa ana a agaluwo nthawi zambiri kumachitika chifukwa chakuti maselo ena a agaluwo sanagwire ntchito yake. Mwachitsanzo, pali agalu enaake amene amakhala ndi miyendo ifupiifupi chifukwa choti minofu yawo yokhala pakati pa mafupa sikula bwinobwino.