Mawu a M'munsi
b M’buku la Genesis, mawu oti “mtundu” amatanthauza zambiri kusiyana ndi zimene asayansi amatanthauza akamanena kuti “mtundu.” Nthawi zambiri asayansi akanena kuti pali “mtundu watsopano wa nyama,” kwenikweni amakhala akunena za nyama ya mtundu womwe ulipo kale kungoti ikusiyana pang’ono ndi zinzake.