Mawu a M'munsi
b Musadzikakamize kulira pofuna kusonyeza kuti muli ndi chisoni. Anthufe timasonyeza chisoni mosiyanasiyana. Koma chofunika kwambiri n’chakuti: Ngati misozi yalengeza, imeneyo ikhoza kukhala “nthawi yolira.”—Mlaliki 3:4.