Mawu a M'munsi
c Chigamulo chimenechi chinatanthauza kuti boma la Bulgaria linafunikanso kupereka mwayi wa ntchito zina zosakhudzana ndi usilikali ngakhale pang’ono kwa anthu onse amene ankakana kulowa usilikali chifukwa cha chikumbumtima chawo.