Mawu a M'munsi
b Pofotokoza za mawu a Satanawa buku lina lofotokozera Baibulo linanena kuti: “Mofanana ndi mmene zinalili pa mayesero oyambirira amene Adamu ndi Hava analephera . . . , nkhani yagona pa kusankha pakati pa kuchita zimene Satana amafuna kapena kuchita zimene Mulungu amafuna, zomwe zikutanthauza kuti munthu akuyenera kusankha mmodzi woti azimulambira. Satana amafuna kuti anthu azimulambira m’malo molambira Mulungu yekha.”