Mawu a M'munsi
d Likasa lopatulika litachotsedwa m’chihema, zikuoneka kuti Yehova ankavomereza nsembe zimene zinkaperekedwa m’malo ena osati kuchihema kokha.—1 Sam. 4:3, 11; 7:7-9; 10:8; 11:14, 15; 16:4, 5; 1 Mbiri 21:26-30.