Mawu a M'munsi
e Zikuoneka kuti Ezekieli anali ndi zaka 30 pamene anayamba kunenera mu 613 B.C.E. Choncho ayenera kuti anabadwa m’chaka cha 643 B.C.E. (Ezek. 1:1) Yosiya anayamba kulamulira mu 659 B.C.E., ndipo buku la Chilamulo, mwina loyambirira lenileni, linapezeka atatsala pang’ono kukwanitsa zaka 18 akulamulira kapena cha m’ma 642-641 B.C.E.