Mawu a M'munsi b Kwa zaka zambiri, mabuku athu akhala akufotokoza makhalidwe osiyanasiyana pafupifupi 50 a Yehova.—Onani Watch Tower Publications Index pamutu wakuti “Jehovah,” komanso kamutu kakang’ono kakuti “Qualities by Name.”