Mawu a M'munsi
b Polola kuti Yerusalemu awonongedwe, Yehova anapereka chiweruzo ku ufumu wa mafuko awiri wa Yuda komanso ufumu wa mafuko 10 wa Isiraeli. (Yer. 11:17; Ezek. 9:9, 10) Onani Insight on the Scriptures, Vol. 1, tsa. 462, “Chronology—From 997 B.C.E. to Desolation of Jerusalem.”