Mawu a M'munsi
a Zaka pafupifupi 200 Ezekieli asanauzidwe ulosiwu, anthu amene ankakhala mu ufumu wa mafuko 10 (“ndodo ya Efuraimu”) anatengedwa ndi Asuri kupita ku ukapolo.—2 Maf. 17:23.