Mawu a M'munsi
c Kachisi wauzimu anayamba kugwira ntchito koyamba mu 29 C.E., pamene Yesu anabatizidwa n’kuyamba ntchito yake ngati Mkulu wa Ansembe. Koma kulambira koyera kunanyalanyazidwa kwa nthawi yaitali padziko lapansi atumwi onse a Yesu atamwalira. Kuyambira mu 1919 m’pamene kulambira koyera kunakwezedwa.