Mawu a M'munsi
c Zikuoneka kuti Babulo Wamkulu akamadzawonongedwa sizikutanthauza kuti anthu onse omwe ali m’zipembedzo zabodza adzaphedwa. Pa nthawiyo, ngakhale atsogoleri ena azipembedzo angadzachoke m’zipembedzo zawo n’kumanena kuti sanali m’zipembedzo zimenezo.—Zek. 13:3-6.