Mawu a M'munsi a Mawu ena a Chiheberi amene amatanthauza kulambira amatanthauzanso “kutumikira.” Choncho kulambira kumaphatikizapo kutumikira.—Eks. 3:12, mawu am’munsi.