Mawu a M'munsi
a Ngati m’lsrayeli anafa pamene mkazi wake asanabale mwana yemwe akalandira cholowa, mbale wake wamwamunayu anayenera kukwatira mkazi wamasiyeyo mchiyang’aniro cha kubala mwana kaamba ka iye.—Deuteronomo 25:5-10.