Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Monga mmene amachitira ambiri lerolino, Huxley anawona kupanda chilungamo kwa Chikristu cha Dziko. Mu nkhani yolembedwa pa kusadziŵa, iye analemba kuti: “Ngati tikanawona kokha . . . mafunde a chinyengo ndi nkhanza, bodza, kupha, kunyalanyaza kwa thayo lirilonse laumunthu, komwe kukuyenda kuchokera ku magwero amenewa limodzi ndi njira ya mbiri yakale ya mitundu Yachikristu, zolingalira zathu zoipa koposa za Helo zikanakhala zozimiririka pambali pa masomphenyawo.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena