Mawu a M'munsi
a Mwachiwonekere, mtundu wa Israyeli unapambana m’luso la kuimba. Chifaniziro chozokota cha Asuri chimasonyeza kuti Mfumu Sanakeribu anafuna oimba Achiisrayeli monga msonkho wochokera kwa Mfumu Hezekiya. Grove’s Dictionary of Music and Musicians imanena kuti: “Kufuna oimba monga msonkho . . . kunali kwachilendo kwambiri.”