Mawu a M'munsi a Tanakh Yachiyuda imati: “AMBUYE apereka lamulo; akazi amene abweretsa mbiri yabwino ali khamu lalikulu.”