Mawu a M'munsi
b Atumiki a nthaŵi yonse a Mboni za Yehova amatchedwa apainiya. Mpainiya wothandiza amathera maola osachepera pa 60 muutumiki mwezi uliwonse, mpainiya wokhazikika maola 90, ndi mpainiya wapadera maola 140.