Mawu a M'munsi
a Pamene kuli kwakuti pali zambiri zimene tingaphunzire, onani zimene inu panokha mungaphunzire ponena za Yesu m’zitsanzo zotsatira zimene zingathandizire umodzi mumpingo wanu: Mateyu 12:1-8; Luka 2:51, 52; 9:51-55; 10:20; Ahebri 10:5-9.