Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Nsanja ya Olonda yachingelezi panthaŵi ina inapereka ndemanga yaluntha yakuti: “Tisawonongere moyo uno pa zinthu zachabechabe . . . Ngati moyo uno ndiwo wokha umene uliko, palibe chinthu chofunika. Uli ngati mpira woponyedwa m’mwamba umene umangogweranso pansi. Uli ngati mthunzi wodutsa, duŵa limene limafota, udzu woti akaudula ufota. . . . Pamiyeso ya nthaŵi yomka muyaya moyo wathu uli ngati kachitsotso kopanda pake. M’kuyenda kwa nthaŵi uli ngati dontho laling’onong’ono. Ndithudi [Solomo] ali bwino popenda nkhaŵa zambiri za moyo wa munthu ndi zochita zake ndi kunena kuti zili chabe. Timapita msanga ndipo ndi bwino kusabadwa nkomwe, mabiliyoni adzafika ndi kupita, oŵerengeka chabe ndiwo amadziŵa kuti tinali pano. Lingaliro limeneli silimasonyeza kupanda chidaliro kapena kusonyeza chisoni kapena kuchititsa mantha. Chili choonadi, chenicheni, lingaliro lenileni, ngati moyo uno ndiwo wokha umene uliko.”​—August 1, 1957, tsamba 472.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena