Mawu a M'munsi
a Zimene anati Mfundo Zisanu za Fundamentalism, zofotokozedwa mu 1895, zinali zakuti “(1) Malemba ngouziridwa kotheratu ndi osalakwa; (2) Yesu Kristu ali mulungu; (3) Kristu anabadwa kwa namwali; (4) Kristu pamtanda anali mtetezi m’malo mwa onse; (5) Kristu anauka m’thupi ndi kuti adzabweranso iye mwini m’thupi padziko lapansi.”—Studi di teologia (Maphunziro a Zaumulungu).