Mawu a M'munsi
a Pamene madzi akufika poti nkuuma kusanduka ayezi, amapepuka nkuyandama pamwamba. Onani masamba 137-8 m’buku la Life—How Did It Get Here? By Evolution or by Creation?, lofalitsidwa ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc.