Mawu a M'munsi
b Dr. Ford anali profesala wa chipembedzo pakoleji yoyendetsedwa ndi tchalitchi ya Pacific Union College ku U.S.A. Mu 1980 atsogoleri a SDA anampatsa tchuti cha miyezi isanu ndi umodzi kuti akaphunzire za chiphunzitsocho, koma iwo anakana zimene anapezazo. Iye anazifalitsa m’buku lakuti Daniel 8:14, the Day of Atonement, and the Investigative Judgment.