Mawu a M'munsi d Mafakitale, maofesi, ndi nyumba zokhalamo zimenezo sindizo kachisi wamkulu wauzimu wa Mulungu kapena nyumba. Kachisi wauzimu wa Mulungu ndiye makonzedwe ake a kulambira koyera. (Mika 4:1) Choncho, sali nyumba yeniyeni padziko lapansi.