Mawu a M'munsi
a Mwachitsanzo, ku United States ambiri amakhala ndi inshuwalansi ya thanzi, ngakhale kuti imeneyi imadula. Mabanja ena a Mboni apeza kuti madokotala ena amakhala ofunitsitsa kupereka machiritso ena osaloĊµetsapo mwazi ngati mabanja ali ndi inshuwalansi ya thanzi. Madokotala ambiri amalandira ndalama yolipidwira inshuwalansi ya machiritso akutiakuti kapena ndalama yolipiridwa ndi boma.