Mawu a M'munsi
b Malinga ndi kunena kwa Mgiriki wakale wodziƔa za malo a dziko Strabo, anthu a ku Seba anali olemera kwambiri. Akuti anali kugwiritsa ntchito golide mowononga popanga mipando, ziwiya zapanyumba, ngakhalenso makoma, zitseko, ndi madenga a nyumba zawo.