Mawu a M'munsi
c Ena amati mawu ameneĊµa amatanthauza kuti mfumu yaikaziyo inachita chigololo ndi Solomo. Nthano zina zimati mpaka anabereka mwana wamwamuna. Komabe, palibe umboni wochirikiza chilichonse cha zimenezi.