Mawu a M'munsi
b Baibulo la The New Testament in the Original Greek, lotembenuzidwa ndi Westcott ndi Hort, linagwiritsidwa ntchito monga maziko a Malemba Achigiriki. Ndipo Baibulo lotembenuzidwa ndi R. Kittel, lakuti Biblia Hebraica n’lomwe linali maziko a Malemba Achihebri.