Mawu a M'munsi
a Mbuyeyo sanapangane ndi akapolo akewo za nthaŵi yeniyeni imene adzabwerako. Chotero, sanafunikire kulongosola zochita zake zonse, komanso sanafunikire kulongosolera akapolo ake chifukwa chimene wafikira panthaŵi yooneka ngati yochedwa imeneyo.