Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

b Zikuoneka kuti anawo anali amisinkhu yosiyanasiyana. Panopo liwu lotembenuzidwa kuti “tiana” likugwiritsidwanso ntchito potchula mwana wamkazi wa Yairo wazaka 12 zakubadwa. (Marko 5:39, 42; 10:13) Koma posimba nkhani yofananayo ya ana, Luka akugwiritsa ntchito liwu lomwe limatanthauzanso makanda.​—Luka 1:41; 2:12; 18:15.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena