Mawu a M'munsi
a Liwulo “matsenga” limagwiritsidwanso ntchito pofuna kutchula matsenga achiphamaso ochitidwa pabwalo lochitira seŵero amene ali olekanitsidwa ndi mitundu ya zamizimu. Onani Galamukani!, ya September 8, 1993, tsamba 12, “Kodi Kuchita Matsenga Kuli ndi Upandu?”