Mawu a M'munsi
c Mu nthaŵi za m’Baibulo mwambo woika mtembo m’manda chinali chochitika chapadera kwambiri. Choncho, kuikidwa m’manda mosatsata mwambo umenewu linali tsoka lalikulu ndipo kaŵirikaŵiri zinali kusonyeza kukanidwa ndi Mulungu.—Yeremiya 25:32, 33.