Mawu a M'munsi
d Mwachitsanzo, Pinehasi anachita mofulumira kuletsa mliri womwe unapha Aisrayeli zikwizikwi, ndipo Davide analimbikitsa anyamata ake anjala kudya naye limodzi mkate woonekera “m’nyumba ya Mulungu”. Mulungu sanatsutse iliyonse ya njira zimenezi kuti kunali kudzikuza.—Mateyu 12:2-4; Numeri 25:7-9; 1 Samueli 21:1-6.