Mawu a M'munsi
b Matenda ena opatsirana mwa kugonana amawononga chiŵindi. Mwachitsanzo, chindoko chikafika poipa, tizilombo toyambitsa matendawo timawononga chiŵindi. Ndipo tizilombo tomwe timayambitsa matenda a chinzonono tingatupitse chiŵindi.