Mawu a M'munsi
a Kayendetsedwe ka zinthu ndi mapepala aboma n’kosiyanasiyana malinga ndi malo ake. Kayendetsedwe ka zinthu zosudzulira zofotokozedwa m’mzikalata zaboma ziyenera kupendedwa mosamala musanasaine. Ngati mwamuna kapena mkazi wosalakwa wasaina mapepala omwe akusonyeza kuti sakutsutsa malingaliro a mnzake akuti asudzulane, zikatanthauza kuti akugwirizana ndi chisudzulocho.—Mateyu 5:37.