Mawu a M'munsi
b Ngakhale kuti mawu achihebri akuti “nzeru” nthaŵi zonse amasonyeza chinthu chachikazi, izi sizitsutsana ndi kuwagwiritsa ntchito kuimira Mwana wa Mulungu. Mawu achigiriki akuti “chikondi” m’mawu akuti “Mulungu ndiye chikondi,” amasonyezanso chinthu chachikazi. (1 Yohane 4:8) Komabe amagwiritsidwa ntchito kuimira Mulungu.