Mawu a M'munsi
a Poyamba maphunziro anali kuchitidwa kumalo amene anthu achidwi anali kusonkhana. Koma posapita nthaŵi, maphunzirowo anayamba kuchitidwanso kwa munthu payekha ndiponso mabanja.—Onani buku la Jehovah’s Witnesses—Proclaimers of God’s Kingdom, tsamba 574, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.