Mawu a M'munsi
a Mawu achigiriki omwe ali pa 1 Petro 4:3, kwenikweni amatanthauza “kupembedza mafano kosaloleka mwalamulo.” Mawuŵa atembenuzidwa mosiyanasiyana m’mabaibulo a Chicheŵa monga “kupembedza koipa kwa mafano,” ndi “kupembedza mafano konyansa.”