Mawu a M'munsi
c Otsutsa ena anena kuti Elamu sanakhalepo ndi mphamvu zoterozo ku Sinara ndipo kuti nkhani yokhudza kuukira kwa Kedorelaomere ndi yonama. Kuti mumve umboni wa zofukula m’mabwinja wovomereza nkhani ya m’Baibuloyi, onani Nsanja ya Olonda ya July 1, 1989, masamba 4-7.