Mawu a M'munsi
b Mapemphero ngati ameneŵa m’malo mwa mwana wamng’ono wochotsedwayo sayenera kuperekedwa poyera pamisonkhano ya mpingo, chifukwa ena mwina sakudziŵa mmene munthuyo akuchitira.—Onani Nsanja ya Olonda ya Chingelezi ya October 15, 1979, tsamba 31.