Mawu a M'munsi
a Makolo ena amatha mantha ndi zinthu zimene zingawavulaze ngati ntchito imene amagwira imawachititsa kukumana ndi zinthu za ngozi nthaŵi zonse. Pamene mmisiri wina yemwe anagwira ntchito yake kwa nthaŵi yaitali anamufunsa chifukwa chimene akalipentala ambiri amakhalira oduka chala, iye anati: “N’chifukwa chakuti amatha mantha ndi masowo a magetsi amphamvu kwambiri.”