Mawu a M'munsi
a Akatswiri ena amakonda kugwiritsa ntchito dzina lakuti “Yahweh” m’malo mwa “Yehova.” Ngakhale zili choncho, otembenuza mabaibulo amakono ambiri achotsa dzina la Mulungu m’mabaibulo awo, ndi kuikamo mayina aulemu omwe angaperekedwe kwa aliyense monga “Ambuye” kapena “Mulungu.” Kuti mudziŵe zambiri zokhudza dzina la Mulungu, onani buku lakuti Dzina la Mulungu Limene Lidzakhala Kosatha, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.