Mawu a M'munsi
a Popeza Yesu alibe tchimo, ubatizo wake sunali chizindikiro cha kulapa machimo. Ubatizo wake unasonyeza kudzipereka kwake kwa Mulungu kuti achite chifuniro cha Atate wake.—Ahebri 7:26; 10:5-10.