Mawu a M'munsi
c Ku France kunachitika misonkhano yaikulu yapadera itatu imene inachitikira m’mizinda ya Paris, Bordeaux, ndi Lyons. Ku Italy, nthumwi zochokera ku United States anazitumiza ku Rome ndi ku Milan, ngakhale kuti misonkhano yaikulu yokwana isanu ndi inayi inachitika panthaŵi imodzi.