Mawu a M'munsi
a Ngakhale kuti Josephus anafotokoza kuti Ayuda anali kulemekeza zinthu zopatulika, iye anafotokozanso lamulo la Mulungu motere: ‘Munthu aliyense asachitire mwano milungu imene anthu a mizinda ina amalambira, ndiponso asalande za mu akachisi, kapena kutenga chuma chimene anachipatulira kwa mulungu wina aliyense.’—Jewish Antiquities, Buku 4, mutu 8, ndime 10.