Mawu a M'munsi
b Mwa khamu lalikulu limene linapezeka pa chikumbutso chapachaka cha Chakudya Chamadzulo cha Ambuye chimene chinachitika pa March 28, 2002, anthu miyandamiyanda sakutumikira Yehova pakalipano. Tikupemphera kuti mitima ya ambiri mwa anthu achidwi ameneĊµa idzalimbikitsidwa posachedwa kuti adzipereke kulandira mwayi wokhala ofalitsa uthenga wabwino.