Mawu a M'munsi
a Ufulu wachipembedzo wa mkazi wake umaphatikizapo kupita kumisonkhano yachikristu. Nthaŵi zina, mwamuna safuna kusamalira ana aang’ono panthaŵi yomwe mkazi wake wapita kumisonkhano, choncho ndi udindo wa mayi wachikondi kupita ndi anawo kumisonkhano.